Mulungu wamanganso Ziyoni ndipo akuitana anthu onse ku Ziyoni chifukwa Mulungu amakhala mu Ziyoni, komanso chifukwa Ziyoni ndi malo amene maphwando a Mulungu a moyo amasungidwira kudzera m’mphwando anthu angathe kulandira chikhulukukiro cha machimmo ndi madalitso a moyo wosatha.
Chifukwa chake, mamembala a Mpingo wa Mulungu amapereka ulemerero ndi mayamiko kwa Mulungu Elohim—Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amai—chifukwa chotsogolera anthu ku Ziyoni yomwe yamangidwanso.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi