Mulungu anatchula chikondi m’mabuku onse 66 a m’Baibulo.
Mulungu anapereka zitsanzo za chikondi chachikulu pobwera ku dziko lapansi, kunyamula machimo onse a anthu, ndipo ngakhale kupachikidwa.
Choncho ana a Mulungu ayenera kukonda, kugwirizana ndi kuganizirana kuti akwaniritse lamulo latsopano ndi kulandira madalitso akumwamba.
Lero, Mamembala a Mpingo wa Mulungu padziko lonse amamvetsetsa zikhalidwe ndi maganizo osiyanasiyana pogwiritsa ntchito chiphunzitso cha chikondi Amaganizirana wina ndi mzake, kusonyeza ulemerero wa Mulungu mwa ntchito zabwino ndi kukonda anansi, monga ziphunzitso za Mulungu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi.
Tsopano mwayeretsa mitima yanu pomvera choonadi, kuti muzikondana ndi abale anu, kukondana kwenikweni kochokera pansi pa mtima. 1 Petro 1:22
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi