Onse aŵiri Yesu mu m'badwo wa Mwana ndi Khristu Ahnsahnghong mu m'badwo wa Mzimu Woyera anabwera padziko lapansi kudzatipatsa moyo. Popeza Mulungu anapatsa anthu amene anataya miyoyo yawo chifukwa cha uchimo Paska wa pangano latsopano, lomwe ndi lamulo la Mzimu wa moyo—kudya thupi ndi mwazi wa Yesu—mamembala onse a Mpingo wa Mulungu padziko lonse lapansi amasunga Paska kukhala wopatulika.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi