Baibulo limanena kuti chifukwa chimene anthu amafera ndi chifukwa cha machimo. Komabe, Baibulo limanenanso kuti ngati alandira chikhululukiro cha machimo, miyoyo yawo ili ndi moyo wosatha ngakhale kuti matupi awo amawonongeka.
Tiyenera kubatizidwa m 'dzina la Mpulumutsi amene ali ndi ulamuliro wokhululukira machimo ndi kupereka moyo wosatha. Mpingo wokha umene umapereka ubatizo m 'dzina la Mulungu Atate, Yehova, Mulungu Mwana, Yesu, ndi Mulungu Mzimu Woyera, Khristu Ahnsahnghong, ndi Mpingo wa Mulungu.
Nyakukunda ndinamchitisa kukhala mzati m'Nyumba ya Mulungu wanga, iyembo nkhabe dzabulukamo tayu. Pana iye ndinalembapo dzina ya Mulungu wanga na dzina ya Mzinda wa Mulungu wanga, ule ndi Yerusalemu wachinchino wakutchitha kudzulu kuna Mulungu wanga. Ndinalemba pontho dzinanga yachinchino pana iye. Chivumbulutso 3:12
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Head Office: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of Korea
Main Church: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of Korea
ⓒ World Mission Society Church of God. All rights reserved. Privacy Policy