Mpingo wa Mulungu ukuyembekeza kuti anthu onse adzalowa mu ufumu wa kumwamba pamodzi, ukupeleka chikondi ndi chimwemwe cha Amai Akumwamba kwa anthu ambiri amene akutopa m’chitaganya kumene kudzikonda kwafala.
Malo a umodzi, ndi mtima wa Amai Akumwamba Akumwamba. Ndi Mtima wa Amai, mamembala a Mpingo wa Mulungu amakhala ogwirizana ndipo amachita ntchito zabwino motsatira ziphunzitso Zake. Mamembala amakonda ndi kulemekeza ena onse monga amadzikondera iwo eni.
(Nkhani yokhudza ziwalo za munthu amene anapeza mkaka wa nkhumba kuti uchiritse matenda a mfumu; chiwalo chilichonse cha thupi lake chinkadzitama kuti n’chapamwamba.)
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi