Nzeru ya Mzimu Woyera yoperekedwa ndi Mulungu singafanane ndi nzeru za anthu a dziko lapansi, motero, iwo amene amasunga pangano latsopano ndiwo anzeru kwambiri.
Masiku ano, mpingo umene umakhulupirira ndi kutsatira pangano latsopano lovumbulutsidwa ndi Khristu Ahnsahnghong komanso Mulungu Amai ndi Mpingo wa Mulungu. Mpingo wa Mulungu wokha ndi umene uli ndi nzeru zauzimu zochitira ntchito zauzimu m’dziko lauzimu, monga chozizwitsa chosandutsa madzi kukhala vinyo pa ukwati waku Kana.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi