Mipingo ina imati angelo amagwira ntchito ngati Mzimu Woyera.
Koma, palibe vesi limodzi m’mabuku onse 66 a Baibulo lomwe
limanena kuti angelo ndi Mzimu, kapena kuti amagwira ntchito
ngati Mzimu. Mtumwi Paulo analemba kuti:
Aheb 1:14 『Kodi siili yonse (angelo) mizimu yotumikira, yotumidwa kuti itumikire iwo amene adzalowa chipulumutso?』
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi