Ulendo wa moyo wanga unali mumdima wathunthu; Sindinathe kuona kapena kumvetsa.
Ndinafunsa kambirimbiri kuti, “Kodi ndinachokera kuti?
Pamene ndinali wotopa ndekha, pamene ndinali wothedwa nzeru, kuunika kwakukulu kunadza kwa ine, kuunika kwa Atate ndi Amayi.
Atate ndi Amayi anandipukuta misozi ndikundikumbatira monyadira ndi chikondi Chawo.
Ndawasowa bwanji Makolo anga a Kumwamba, Mikono yawo yachikondi ikundikumbatira!
Makolo Anga a Kumwamba, Munandipeza ndipo munandikhululukira machimo anga onse aakulu!
Mayamiko ndi matamando onse apite kwa Inu!
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi